Job 27:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyumba imene akuimanga ili ngati ukonde wa kangaude, ili ngati msasa umene mlonda amamanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amanga nyumba yake ngati kangaude, ndi ngati wolindira amanga dindiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyumba imene akuyimanga ili ngati mokhala kadziwotche, ili ngati msasa umene mlonda amamanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amanga nyumba yace ngati kadzoce, Ndi ngati wolindira amanga dindiro.