Job 27:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amapita ku bedi ali wolemera, koma kutha kwake nkumeneko, poti aphenyule maso, angoona chuma chakecho pali ng'wa!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Agona pansi ali wachuma, koma saikidwa; potsegula maso ake, wafa chikomo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amapita kokagona ali wolemera koma kutha kwake nʼkomweko; akatsekula maso ake, chuma chake chonse chapita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Agona pansi ali wacuma, koma saikidwa; Potsegula maso ace, wafa cikomo,