Job 27:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pali Mulungu wamoyo amene wakana kundiweruza molungama, pali Mphambe amene wandipweteketsa mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pali Mulungu, amene anandichotsera zoyenera ine, ndi Wamphamvuyonse, amene anawawitsa moyo wanga,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndithu pali Mulungu wamoyo, amene wakana kundiweruza molungama, Wamphamvuzonse, amene wawawitsa mtima wanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pali Mulungu, amene anandicotsera zoyenera ine, Ndi Wamphamvuyonse, amene anawawitsa moyo wanga,