Job 27:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imakuntha pa iye osamchitira chifundo, pamene iye akuyesa kuithaŵa mwaliŵiro.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Mulungu adzamponyera zoopsa, osamleka; kuthawa akadathawa m'dzanja lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imakuntha pa iye osamuchitira chisoni, pamene akuyesa kuthawa mphamvu zake mwaliwiro.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Mulungu adzamponyera zoopsa, osanlieka; Kuthawa akadathawa m'dzanja lace.