Job 27:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi zonse pamene ndikupumabe, Mulungu namandipatsa mpweya wa moyo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti moyo wanga wonse ukali mwa ine, ndi mpweya wa Mulungu m'mphuno mwanga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nthawi zonse pamene ndili ndi moyo, mpweya wa Mulungu uli mʼmphuno mwanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti moyo wanga wonse ukali mwa ine, Ndi mpweya wa Mulungu m'mphuno mwanga;