Job 27:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zakuti mukunena zoona, ine sindikuvomera. Kunena za ine ndidzakhalabe wokhulupirika mpaka kufa kwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sindivomereza konse kuti muli olungama; mpaka kufa ine sinditaya ungwiro wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sindidzavomereza kuti inu mukunena zoona; mpaka imfa yanga, sindidzataya ungwiro wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sindibvomereza konse kuti muli olungama; Mpaka kufa ine sinditaya ungwiro wanga.