Job 27:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sindidzaleka kunena kuti ndine wolungama, sindidzasintha maganizo anga. Mtima wanga sukunditsutsa pa chinthu chilichonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiumirira chilungamo changa, osachileka; chikhalire moyo ine, mtima wanga sunditonza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzasunga chilungamo changa ndipo sindidzalola kuti chindichokere; chikumbumtima changa sichidzanditsutsa nthawi yonse ya moyo wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiumirira cilungamo canga, osacileka; Cikhalire moyo ine, mtima wanga sunditonza.