Job 27:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Adani anga ziŵaonekere zinthu zoyenerera anthu oipa. Ondiwukira alangidwe monga momwe amachitira osalungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mdani wanga akhale ngati woipa, ndi iye amene andiukira ngati wosalungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mdani wanga akhale ngati woyipa, wondiwukira akhale ngati munthu wosalungama!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mdani wanga akhale ngati woipa, Ndi iye amene andiukira ngati wosalungama.