Job 28:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Phompho likuti, ‘Sizipezeka mwa ine muno,’ nyanja ikuti, ‘Mwa ine munonso ai.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pozama pakuti, Mwa ine mulibe; ndi nyanja ikuti, Kwa ine kulibe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Phompho likuti, ‘Sizipezeka mwa ine muno.’ Nyanja ikuti, ‘Mwa ine munonso ayi.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pozama pakuti, Mwa ine mulibe; Ndi nyanja ikuti, Kwa ine kulibe.