Job 28:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale golide wokoma kwambiri wa ku Ofiri sangafike pa mtengo wa nzeruzo, miyala ya onikisi kapena ya safiro nayonso singafikepo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sailinganiza ndi golide wa Ofiri, ndi sohamu wa mtengo wake wapatali kapena safiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nzeru singagulidwe ndi golide wa ku Ofiri, kapena ndi miyala ya onikisi kapena ya safiro.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sailinganiza ndi golidi wa Ofiri, Ndi sohamu wa mtengo wace wapatali kapena safiro.