Job 28:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtengo wake wa nzeru ndi woposa miyala ya korali ndi krisitala, umapambananso ndi miyala ya rubi yomwe. Mtengo wake wa nzeru umapambana ndi ngale zomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Korali kapena ngale sizikumbukikapo. Mtengo wake wa nzeru uposa wa korali wofiira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Miyala ya korali ndi krisitali siyoyeneranso ndi kuyitchula nʼkomwe; mtengo wa nzeru ndi woposa miyala ya rubi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Korali kapena ngale sizikumbukikapo. Mtengo wace wa nzeru uposa wa korali wofiira.