Job 28:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chitsulo amachikumba pansi, mkuŵa amachita kuusungunula ku miyala yamkuŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chitsulo achitenga m'nthaka, ndi mkuwa ausungunula kumwala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chitsulo amachikumba pansi, ndipo mkuwa amawusungunula ku miyala yamkuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Citsulo acitenga m'nthaka, Ndi mkuwa ausungunula kumwala.