Job 28:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mulungu yekha ndiye amadziŵa njira yake yopita kumeneko, amadziŵa kumene nzeruzo zimakhala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu ndiye azindikira njira yake, ndiye adziwa pokhala pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu yekha ndiye amadziwa njira yake yopita kumeneko, ndipo Iye yekha amadziwa kumene nzeru imakhala,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu ndiye: azindikira njira yace, Ndiye adziwa pokhala pace.