Job 28:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamene adakhazika lamulo loti mvula izigwa, nakonza njira za ching'aning'ani cha bingu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuchitira mvula lamulo, ndi njira yoyendamo mphezi ya bingu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
atakhazikitsa lamulo loti mvula izigwa ndi kukonza njira ya chingʼaningʼani cha bingu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakucitira mvula lamulo, Ndi njira yoyendamo mphezi ya bingu;