Job 28:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amaloŵa mu mdima atatenga nyale namafunafuna miyalayo mpaka ku malire a mgodiwo, akuyenda mu mdima wandiweyani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu athawitsa mdima, nafunafuna mpaka malekezero onse, miyala ya mdima wa bii ndi ya mthunzi wa imfa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu amalowa mu mdima atatenga nyale, amafunafuna miyala mpaka ku malire a mgodiwo, kufuna mkuwa mu mdima wandiweyani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu athawitsa mdima, Nafunafuna mpaka malekezero onse, Miyala ya mdima wa bii ndi ya mthunzi wa imfa.