Job 28:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaka imatulutsa chakudya, koma kunsi kwake kumachita ngati kofwantchuka ndi moto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena za nthaka, kuchokera momwemo mumatuluka chakudya, ndi m'munsi mwake musandulizika ngati ndi moto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthaka, imene imatulutsa zakudya, kunsi kwake kumachita ngati kwasandulizika ndi moto;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena za nthaka, kucokera momwemo mumaturuka cakudya, Ndi m'munsi mwace musandulizika ngati ndi moto.