Job 28:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Njira ya mu mgodi imeneyi, palibe mbalame yodya zinzake imene imaidziŵa, kamtema yemwe sanaiwone.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Njira imeneyi palibe chiombankhanga chiidziwa; lingakhale diso la kabawi losapenyapo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe mbalame yodya zinzake imene imadziwa njira yobisikayi, palibe kamtema amene anayiona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Njira imeneyi palibe ciombankhanga ciidziwa; Lingakhale diso la kabawi losapenyapo.