Job 28:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu amaphwanya matanthwe olimba, amagadabula mapiri kuyambira m'tsinde.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu atambasulira dzanja lake kumwala; agubuduza mapiri kuyambira kumizu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu amaphwanya matanthwe olimba, ndipo amagubuduza mapiri kuyambira mʼtsinde.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu atambasulira dzanja lace kumwala; Agubuduza mapiri kuyambira kumizu.