Job 29:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zidatero chifukwa choti ndinkapulumutsa amphaŵi olira, ndinkalanditsa ana amasiye opanda woŵathandiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndinapulumutsa wozunzika wakufuula; mwana wamasiye yemwe wosowa mthandizi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa ndinkapulumutsa mʼmphawi wofuna chithandizo, ndiponso mwana wamasiye amene analibe aliyense womuthandiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndinapulumutsa wozunzika wakupfuula; Mwana wamasiye yemwe wosowa mthandizi.