Job 29:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene anali pa zoopsa kwambiri ankanditamanda, akazi amasiye ndinkaŵasangalatsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dalitso la iye akati atayike linandidzera, ndi mtima wa mkazi wamasiye ndinauimbitsa mokondwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu amene anali pafupi kufa ankandidalitsa; ndinkasangalatsanso mkazi wamasiye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dalitso la iye akati atayike linandidzera, Ndi mtima wa mkazi wamasiye ndinauyimbitsa mokondwera.