Job 29:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi zonse ndinkachita zoyenera, ntchito zanga zonse zinali zangwiro.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinavala chilungamo, ndipo chinandivala ine; chiweruzo changa chinanga mwinjiro ndi nduwira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chilungamo chinali ngati chovala changa; chiweruzo cholungama ndiye chinali mkanjo ndi nduwira yanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinabvala cilungamo, ndipo cinandibvala ine; Ciweruzo canga cinanga mwinjiro ndi nduwira.