Job 29:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Osauka ndinali ngati bambo wao, anthu osaŵadziŵa konse ndinali mtetezi wao pa milandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinali atate wa waumphawi; ndi mlandu wa iye amene sindinamdziwa ndinafunsitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinali ngati abambo kwa anthu aumphawi; ndinkayimira mlendo pa mlandu wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinali atate wa waumphawi; Ndi mlandu wa iye amene sindinamdziwa ndinafunsitsa.