Job 29:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinkaononga mphamvu za anthu ankhalwe, ndinkalanditsa amene anali atagwidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinathyola nsagwada ya wosalungama, ndi kukwatula chogwidwa kumano kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinkawononga mphamvu za anthu oyipa ndi kulanditsa amene anali atagwidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinatyola nsagwada ya wosalungama, Ndi kukwatula cogwidwa kumano kwace.