Job 29:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono mumtimamu ndinkati, ‘Ndidzafera pakati pa ana anga, masiku a moyo wanga ndidzaŵachulukitsa kwambiri ngati mchenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ndinati, Ndidzatsirizika m'chisa changa; ndipo ndidzachulukitsa masiku anga ngati mchenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndinkaganiza kuti, ‘Ndidzafera mʼnyumba yanga, masiku a moyo wanga ali ochuluka ngati mchenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndinati, Ndidzatsirizika m'cisa canga; Ndipo ndidzacurukitsa masiku anga ngati mcenga.