Job 29:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinali ngati mtengo umene mizu yake yatambalalira ku madzi umene masamba ake ndi onyowa ndi mame.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muzu wanga watambalala kufikira kumadzi; ndi mame adzakhala pa nthambi yanga usiku wonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mizu yanga idzatambalalira ku madzi, ndipo mame adzakhala pa nthambi zanga usiku wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muzu wanga watambalala kufikira kumadzi; Ndi mame adzakhala pa nthambi yanga usiku wonse.