Job 29:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense ankandilemekeza, nthaŵi zonse mphamvu zanga zinali ngati uta wolimba.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ulemu wanga udzakhala wosaguga mwa ine, ndi uta wanga udzakhala wosalifuka m'dzanja mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ulemerero wanga udzakhala wosaguga mwa ine, ndipo uta wanga udzakhala watsopano nthawi zonse mʼdzanja langa.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ulemu wanga udzakhala wosaguga mwa ine, Ndi uta wanga udzakhala wosalifuka m'dzanja mwanga.