Job 29:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankayembekeza ine monga momwe amayembekezera mvula, ankangoti kukamwa yasa ngati anthu odikira mvula yam'malimwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anandilindira ngati kulindira mvula, nayasama pakamwa pao ngati kulira mvula ya masika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ankayembekezera ine monga momwe amayembekezera mvula ndipo ankalandira mawu anga ngati mvula ya mʼmalimwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandilindira ngati kulindira mvula, Nayasama pakamwa pao ngati kulira mvula ya masika.