Job 29:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinkaŵasekerera pamene iwowo analibenso chikhulupiriro, kukoma mtima kwanga kunkaŵalimbitsa mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinawaseka akapanda kulimbika mtima; ndipo sanagwetse kusangalala kwa nkhope yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikawasekerera, iwo sankatha kukhulupirira; kuwala kwa nkhope yanga chinali chinthu chamtengowapatali kwa iwowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinawaseka akapanda kulimbika mtima; Ndipo sanagwetsa kusangalala kwa nkhope yanga.