Job 29:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinkasankhula njira yao, ndipo ndinkaŵatsogolera ngati mfumu, tsono ndidakhazikika pakati pao, ngati mfumu pakati pa ankhondo ake, ndinali ngati msangalatsi pakati pa olira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinawasankhira njira yao ndi kukhala mkulu wao. Ndinakhala ngati mfumu mwa ankhondo ake, ngati wotonthoza ofedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinkawasankhira njira yawo ndipo ndinkawatsogolera ngati mfumu; ndinkakhala ngati mfumu pakati pa gulu lake lankhondo; ndinali ngati msangalatsi pakati pa anthu olira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinawasankhira njira yao ndi kukhala mkuru wao. Ndinakhala ngati mfumu mwa ankhondo ace, Ngati wotonthoza ofedwa.