Job 29:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo Mulungu anali nane, nyale yake inkandiwunikira mu mdima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
muja nyali yake inawala pamutu panga, ndipo ndi kuunika kwake ndinayenda mumdima;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamene nyale yake inkandiwunikira ndipo ndi kuwunika kwakeko ine ndinkatha kuyenda mu mdima!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muja nyali yace inawala pamutu panga, Ndipo ndi kuunika kwace ndinayenda mumdima;