Job 29:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Masiku amenewo ndinali pabwino zedi, madalitso a Mulungu anali pabanja panga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga umo ndinakhala m'masiku anga olimba, muja uphungu wa Mulungu unakhala pahema panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithu, masiku amene ndinali pabwino kwambiri, pamene ubwenzi wa Mulungu unkabweretsa madalitso pa nyumba yanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga umo ndinakhala m'masiku anga olimba, Muja uphungu wa Mulungu unakhala pahema panga;