Job 29:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo ng'ombe ndi mbuzi zanga zinkandipatsa mkaka wambiri, mitengo yanga ya olivi inkamera ndi m'matanthwe momwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
muja popondera ine padakhatamira ndi mafuta amkaka, ndi thanthwe linanditsanulira mitsinje ya mafuta a azitona!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamene popondapo ine panali patakhathamira mafuta a mkaka, ndipo pa thanthwe pamatuluka mitsinje ya mafuta a olivi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muja popondera ine padakhatamira ndi mafuta amkaka, Ndi thanthwe linanditsanulira mitsinje ya mafuta aazitona!