Job 3:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku limenelo litembereredwe, chifukwa ndi limene ndidatuluka m'mimba mwa mai wanga, ndipo ndi limene lidandiwonetsa zovuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popeza sunatseka pa makomo ake mimba ya mai wanga. Kapena kundibisira mavuto pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti tsiku limenelo ndiye ndinatuluka mʼmimba ya amayi anga ndipo ndi limene linandionetsa zovuta.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza sunatseka pa makomo ace mimba ya mai wanga. Kapena kundibisira mabvuto pamaso panga.