Job 3:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Bwanji sindidangobadwa wofaifa! Bwanji sindidangoti badwu nkufa!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinalekeranji kufera m'mimba? Ndi kupereka mzimu wanga pobadwa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Bwanji ine sindinawonongeke pamene ndinkabadwa ndi kufa pamene ndimatuluka mʼmimba?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinalekeranji kufera m'mimba? Ndi kupereka mzimu wanga pobadwa ine?