Job 3:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani mai wanga adandifukata? Chifukwa chiyani adandiyamwitsa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anandilandiriranji maondo? Kapena mawere kuti ndiyamwe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani panali mawondo wondilandirirapo ndi mawere woti andiyamwitsepo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandilandiriranji maondo? Kapena mabere kuti ndiyamwe?