Job 3:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwenzi ndikukhala limodzi ndi mafumu ndi aphungu a pa dziko lapansi, amene adadzimangira nyumba zikuluzikulu pa mabwinja akale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamodzi ndi mafumu ndi maphungu a padziko, akudzimangira m'mabwinja;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamodzi ndi mafumu ndi aphungu a dziko lapansi, amene anadzimangira nyumba zikuluzikulu zimene tsopano ndi mabwinja,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamodzi ndi mafumu ndi maphungu a padziko, Akudzimangira m'mabwinja;