Job 3:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwenzi sindidangokhala ngati mtayo woikidwa m'manda, ngati makanda amene sadaonepo kuŵala kwa dzuŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kapena ngati nsenye yobisika ndikadakhala kuli zii; ngati makanda osaona kuunika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kapena, bwanji sindinakwiriridwe pansi monga mwana wobadwa wakufa kale, ngati khanda limene silinaone kuwala kwa dzuwa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena ngati nsenye yobisika ndikadakhala kuli zi; Ngati makanda osaona kuunika.