Job 3:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chifukwa chiyani dzuŵa limamuŵalira munthu wapamavuto? Chifukwa chiyani amakhalabe ndi moyo munthu wa mtima woŵaŵa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amninkhiranji kuunika wovutika, ndi moyo kwa iye wakuwawa mtima,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Chifukwa chiyani dzuwa limawalira iwo amene ali pa mavuto, ndipo moyo umapatsidwa kwa owawidwa mtima,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amninkhiranji kuunika wobvutika, Ndi moyo kwa iye wakuwawa mtima,