Job 3:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amalakalaka imfa, koma osaiwona, amaifunafuna kupambana chuma chobisika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wakuyembekezera imfa, koma kuli zii, ndi kuikumba koposa chuma chobisika,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kwa iwo amene amalakalaka imfa imene sibwera, amene amayifunafuna imfayo kupambana chuma chobisika,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wakuyembekezera imfa, koma kuli zi, Ndi kuikumba koposa cuma cobisika,