Job 3:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amakondwa ndi kusangalala kwambiri akafa ndi kuikidwa m'manda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wakusekerera ndi chimwemwe ndi kukondwera pakupeza manda?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene amakondwa ndi kusangalala akamalowa mʼmanda?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wakusekerera ndi cimwemwe Ndi kukondwera pakupeza manda?