Job 3:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani moyo umapatsidwa kwa munthu amene njira ya moyo wake yabisika, amene Mulungu wamzinga ndi mavuto ponseponse?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amuonetseranji kuunika munthu wa njira yobisika, amene wamtsekera Mulungu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifuwa chiyani moyo umaperekedwa kwa munthu amene njira yake yabisika, amene Mulungu wamuzinga ponseponse?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amuonetseranji kuunika munthu wa njira yobisika, Amene wamtsekera Mulungu?