Job 3:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'malo moti ndidye, ndimalira, ndipo kubuula kwanga nkosalekeza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndikati ndidye, kumadza kuusa moyo kwanga; ndi kudzuma kwanga kumathiridwa ngati madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmalo moti ndidye, ndimalira, ndi kubuwula kwanga nʼkosalekeza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndikati ndidye, kumadza kuusa moyo kwanga; Ndi kudzuma kwanga kumathiridwa ngati madzi.