Job 30:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma tsopano akundiyesa chinthu chochiseka, anthu amene ali ana kwa ine, anthu oti ndi atate ao omwe sindikadaŵayesa oyenera kuti athandizane ndi agalu kuŵeta nkhosa zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tsopano iwo osafikana msinkhu wanga andiseka, iwo amene atate ao ndikadawapeputsa, osawaika pamodzi ndi agalu olinda nkhosa zanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma tsopano akundinyoza, ana angʼonoangʼono kwa ine, anthu amene makolo awo sindikanawalola kuti azithandizana ndi agalu anga kuweta nkhosa zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tsopano iwo osafikana msinkhu wanga andiseka, Iwo amene atate ao ndikadawapeputsa, osawaika pamodzi ndi agaru olinda nkhosa zanga.