Job 30:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Poti Mulungu adandifooketsa ndi kundichepetsa, iwowo adalekeratu kundiwopa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anamasula nsinga zao, nandizunza; anataya chomangira m'kamwa mwao pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano pakuti Mulungu wakhwefula uta wanga ndipo wandisautsa, iwowo analekeratu kundiopa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anamasula nsinga zao, nandizunza; Anataya comangira m'kamwa mwao pamaso panga.