Job 30:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akunditsekera njira, ndipo akufuna kundichititsa ngozi, palibe wina aliyense woŵaletsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aipsa njira yanga, athandizana ndi tsoka langa; ndiwo anthu omwewo osowa mthandizi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anditsekera njira; akufuna kundichititsa ngozi, popanda wina aliyense wowaletsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aipsa njira yanga, Athandizana ndi tsoka langa; Ndiwo anthu omwewo osowa mthandizi.