Job 30:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsopano mtima wanga wachokamo. Ndili pa mavuto, ndilibe popumira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano moyo wanga udzitsanulira m'kati mwanga; masiku akuzunza andigwira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndipo tsopano mtima wanga wachokamo; ndili mʼmasiku amasautso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano moyo wanga udzitsanulira m'kati mwanga; Masiku akuzunza andigwira.