Job 30:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafupa anga akuphwanya usiku, zoŵaŵa sizikuleka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyengo ya usiku mafupa anga awaza mwa ine, ndi zowawa zondikungudza sizipuma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafupa anga akuphwanya usiku pakuti zowawa zanga sizikuleka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyengo ya usiku mafupa anga awaza mwa ine, Ndi zowawa zondikungudza sizipuma.