Job 30:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chovala changa chakwinyikakwinyika chifukwa cha matenda, chikundithina ngati khosi la mkanjo wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa mphamvu yaikulu ya nthenda yanga chovala changa chinasandulika, chindithina ngati pakhosi pa malaya anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmphamvu zake Mulungu wakhala ngati chovala changa; Iye wandigwira ngati chovala chondithina pa khosi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa mphamvu yaikuru ya nthenda yanga cobvala canga cinasandulika, Cindithina ngati pakhosi pa maraya anga.