Job 30:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndimalira kwa Inu Mulungu, koma simundiyankha. Ndimapemphera, koma inu simundiyang'anako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndifuula kwa Inu, koma simundiyankha; ndinyamuka, ndipo mungondipenyerera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Inu Mulungu, ine ndikulirira kwa Inu, koma simukundiyankha; ndikayimirira, Inu simundiyangʼana nʼkomwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipfuula kwa Inu, koma simundiyankha; Ndinyamuka, ndipo mungondipenyerera.