Job 30:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwandichita zankhanza, mwandizunza ndi dzanja lanu lamphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwasandulika kundichitira nkharwe; ndi mphamvu ya dzanja lanu mundizunza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inuyo mumandichitira zankhanza; mumandizunza ndi dzanja lanu lamphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwasandulika kundicitira nkharwe; Ndi mphamvu ya dzanja lanu mundizunza.